Piksy Maloto Video

  • Ndinalota maloto otsekemera ine, inde
    Mwana wanga atafanana nawe ndendende, iwe
    Ngati ndisadzuke
    Usadzandikhumudwitse ey
    Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera

    Category : Malawi Music Videos

    #piksy#maloto#video

    0 Comments and 0 replies
arrow_drop_up